Yoswa 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mizinda ya kumapeto kwa gawo la fuko la Yuda, chakumalire ndi Edomu+ kumʼmwera, inali Kabizeeli, Ederi, Yaguri, Yoswa 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Lebaoti, Silihimu, Aini ndi Rimoni.+ Mizinda 29 pamodzi ndi midzi yake.
21 Mizinda ya kumapeto kwa gawo la fuko la Yuda, chakumalire ndi Edomu+ kumʼmwera, inali Kabizeeli, Ederi, Yaguri,