Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pa tsikuli Yowasi anapatsa Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala* nʼkunena kuti: “Baala adziteteze yekha, chifukwa munthu wina wamugwetsera guwa lake lansembe.” 1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+
32 Pa tsikuli Yowasi anapatsa Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala* nʼkunena kuti: “Baala adziteteze yekha, chifukwa munthu wina wamugwetsera guwa lake lansembe.”
11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+