Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+
32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+