1 Mafumu 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pofika masana Eliya anayamba kuwaseka+ ndipo anali kunena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina watanganidwa ndi zinazake, kapena wapita kuchimbudzi.+ Mwinanso wagona, ndipo muyenera kum’dzutsa.”+
27 Pofika masana Eliya anayamba kuwaseka+ ndipo anali kunena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina watanganidwa ndi zinazake, kapena wapita kuchimbudzi.+ Mwinanso wagona, ndipo muyenera kum’dzutsa.”+