Oweruza 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho, Aisiraeli anagonjetsa Amidiyani,+ ndipo Amidiyaniwo anasiya kulimbana nawo.* Zitatero, dziko linakhala pa mtendere zaka 40 mʼmasiku a Gidiyoni.+
28 Choncho, Aisiraeli anagonjetsa Amidiyani,+ ndipo Amidiyaniwo anasiya kulimbana nawo.* Zitatero, dziko linakhala pa mtendere zaka 40 mʼmasiku a Gidiyoni.+