Oweruza 8:30, 31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Gidiyoni anali ndi ana 70,* chifukwa anali ndi akazi ambiri. 31 Analinso ndi mkazi wamngʼono ku Sekemu, amene anamuberekera mwana wamwamuna, ndipo anamʼpatsa dzina lakuti Abimeleki.+
30 Gidiyoni anali ndi ana 70,* chifukwa anali ndi akazi ambiri. 31 Analinso ndi mkazi wamngʼono ku Sekemu, amene anamuberekera mwana wamwamuna, ndipo anamʼpatsa dzina lakuti Abimeleki.+