Oweruza 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nayenso mdzakazi* wake wa ku Sekemu, anamubalira mwana wamwamuna, ndipo anamutcha dzina lakuti Abimeleki.+
31 Nayenso mdzakazi* wake wa ku Sekemu, anamubalira mwana wamwamuna, ndipo anamutcha dzina lakuti Abimeleki.+