Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pa tsikuli Yowasi anapatsa Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala* nʼkunena kuti: “Baala adziteteze yekha, chifukwa munthu wina wamugwetsera guwa lake lansembe.”
32 Pa tsikuli Yowasi anapatsa Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala* nʼkunena kuti: “Baala adziteteze yekha, chifukwa munthu wina wamugwetsera guwa lake lansembe.”