Oweruza 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yotamu atauzidwa zimene zinachitikazo, nthawi yomweyo anapita pamwamba pa phiri la Gerizimu+ nʼkulankhula mofuula kuti: “Ndimvereni, inu atsogoleri a ku Sekemu, ndipo mukatero Mulungu akumverani. Oweruza 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ngati si choncho, moto utuluke mwa Abimeleki nʼkuwotcha atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo,+ komanso moto utuluke mwa atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo nʼkuwotcha Abimeleki.”+
7 Yotamu atauzidwa zimene zinachitikazo, nthawi yomweyo anapita pamwamba pa phiri la Gerizimu+ nʼkulankhula mofuula kuti: “Ndimvereni, inu atsogoleri a ku Sekemu, ndipo mukatero Mulungu akumverani.
20 Koma ngati si choncho, moto utuluke mwa Abimeleki nʼkuwotcha atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo,+ komanso moto utuluke mwa atsogoleri a ku Sekemu ndi ku Beti-milo nʼkuwotcha Abimeleki.”+