-
Oweruza 17:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Mika anamʼfunsa kuti: “Wachokera kuti?” Iye anayankha kuti: “Ndine Mlevi, ndachokera ku Betelehemu wa ku Yuda ndipo ndikufufuza malo okhala.” 10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Bwanji uzikhala ndi ine ndipo ukhale mlangizi* komanso wansembe wanga? Ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, zovala komanso chakudya.” Atatero Mleviyo analowa mʼnyumba.
-