Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+ Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+ Salimo 63:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa inu mumandithandiza,+Ndipo ndimafuula mosangalala mumthunzi wa mapiko anu.+
7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+ Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+