1 Samueli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzanja la Yehova linayamba kukhaulitsa anthu a ku Asidodi, ndipo linachititsa kuti anthu amumzinda wa Asidodi komanso madera ake ozungulira ayambe kudwala matenda a mudzi.*+ 1 Samueli 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atafika nalo kumeneko, dzanja la Yehova linakhaulitsanso anthu amumzindawo moti anasowa mtendere. Iye anachititsa kuti anthu onse a mumzindawo, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, adwale matenda a mudzi.+
6 Dzanja la Yehova linayamba kukhaulitsa anthu a ku Asidodi, ndipo linachititsa kuti anthu amumzinda wa Asidodi komanso madera ake ozungulira ayambe kudwala matenda a mudzi.*+
9 Atafika nalo kumeneko, dzanja la Yehova linakhaulitsanso anthu amumzindawo moti anasowa mtendere. Iye anachititsa kuti anthu onse a mumzindawo, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, adwale matenda a mudzi.+