Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Davide anathawa nʼkukafika kwa Samueli ku Rama+ ndipo anafotokozera Samueli zonse zimene Sauli anamuchitira. Kenako Davide ndi Samueli anachoka nʼkukakhala ku Nayoti.+

  • 1 Samueli 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ nʼkuthawira kuphanga la Adulamu.+ Azichimwene ake ndi anthu onse amʼnyumba ya bambo ake atamva zimenezi, ananyamuka nʼkumutsatira.

  • 1 Samueli 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Patapita nthawi, Gadi,+ yemwe anali mneneri, anauza Davide kuti: “Usakhalenso kumalo ovuta kufikako. Chokako kumeneko ndipo upite mʼdziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachoka nʼkupita kunkhalango ya Hereti.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena