-
1 Samueli 21:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zitatero Akisi anauza atumiki ake kuti: “Simukuona kuti munthuyu ndi wamisala? Ndiye nʼchifukwa chiyani mwabwera naye kwa ine?
-
-
1 Samueli 27:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Akisi ankamukhulupirira Davide, ndipo mumtima mwake ankati: ‘Ndithu, Davide wakhala ngati fungo lonunkha kwa Aisiraeli anzake, ndipo adzakhalabe mtumiki wanga.’
-