1 Samueli 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, ndipo Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe wa ku Yezereeli.+ 1 Samueli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye nʼkubwerera kudziko la Afilisiti. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+
29 Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, ndipo Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe wa ku Yezereeli.+
11 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye nʼkubwerera kudziko la Afilisiti. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+