Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+ Ekisodo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense amene wamenya munthu mpaka munthuyo kufa ayenera kuphedwa.+ Numeri 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo nʼkufa, ameneyo ndi wopha munthu. Ndipo wopha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+ Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha.
6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+
16 Koma ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo nʼkufa, ameneyo ndi wopha munthu. Ndipo wopha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+
30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha.