2 Samueli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo la Isiraeli+ ndipo Benaya+ mwana wa Yehoyada+ ankatsogolera Akereti ndi Apeleti.+ 1 Mbiri 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Yowabu+ mwana wa Zeruya ndi amene anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.
23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo la Isiraeli+ ndipo Benaya+ mwana wa Yehoyada+ ankatsogolera Akereti ndi Apeleti.+
6 Choncho Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Yowabu+ mwana wa Zeruya ndi amene anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.