2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi ankalemba zimene zachitika. 2 Samueli 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Iwe ndi ine ndife magazi amodzi. Mulungu andilange mowirikiza ngati sindikuika kukhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo mʼmalo mwa Yowabu.’”+
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi ankalemba zimene zachitika.
13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Iwe ndi ine ndife magazi amodzi. Mulungu andilange mowirikiza ngati sindikuika kukhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo mʼmalo mwa Yowabu.’”+