Salimo 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,*+Uzimudalira ndipo iye adzakuthandiza.+ Salimo 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi mphamvu zanu tidzathamangitsa adani athu.+Mʼdzina lanu tidzagonjetsa anthu amene akutiukira.+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu ndi msampha,*+Koma amene amakhulupirira Yehova adzatetezedwa.+