Salimo 78:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Anachititsa kuti malo ake opatulika akhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba,*+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+ Salimo 132:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka.
69 Anachititsa kuti malo ake opatulika akhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba,*+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+
13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka.