Salimo 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu ali mumzindawo+ ndipo sungagonjetsedwe. Mulungu adzauthandiza mʼbandakucha.+ Yesaya 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwezi wathunthu udzachita manyazi,Ndipo dzuwa lowala lidzachita manyazi,+Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wakhala Mfumu+ mʼphiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu,Ulemerelo wake waonekera pamaso pa achikulire a anthu ake.*+
23 Mwezi wathunthu udzachita manyazi,Ndipo dzuwa lowala lidzachita manyazi,+Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wakhala Mfumu+ mʼphiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu,Ulemerelo wake waonekera pamaso pa achikulire a anthu ake.*+