Salimo 67:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti njira zanu zidziwike padziko lonse lapansi,+Kuti mitundu yonse ya anthu idziwe kuti ndinu Mpulumutsi.+ Salimo 102:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitundu ya anthu idzaopa dzina lanu, inu Yehova,Ndipo mafumu onse apadziko lapansi adzaopa ulemerero wanu.+
2 Kuti njira zanu zidziwike padziko lonse lapansi,+Kuti mitundu yonse ya anthu idziwe kuti ndinu Mpulumutsi.+
15 Mitundu ya anthu idzaopa dzina lanu, inu Yehova,Ndipo mafumu onse apadziko lapansi adzaopa ulemerero wanu.+