Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Salimo 130:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Ya,* mukanakhala kuti mumayangʼanitsitsa* zolakwa,Ndi ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+ Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+ Aroma 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Popeza anthu onse ndi ochimwa ndipo amalephera kusonyeza bwinobwino ulemerero wa Mulungu.+ 1 Yohane 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tikamanena kuti, “Tilibe uchimo,” ndiye kuti tikudzinamiza+ ndipo mumtima mwathu mulibe choonadi.
5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+