Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono.”+

  • Yoswa 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Palibe amene adzakugonjetse masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe ngati mmene ndinakhalira ndi Mose+ ndipo sindidzakutaya kapena kukusiya.+

  • 2 Mbiri 32:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu. Musachite mantha kapena kuopa mfumu ya Asuri+ ndi gulu lalikulu limene ali nalo, chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.+

  • Salimo 46:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ali ndi ife.+

      Mulungu wa Yakobo ndi malo athu othawirako otetezeka.* (Selah)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena