Deuteronomo 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mudzawotche pamoto zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Musadzalakelake siliva ndi golide wawo kapena kutenga zinthu zimenezi kuti zikhale zanu,+ kuopera kuti zingakutchereni msampha, chifukwa zinthu zimenezi ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.+
25 Mudzawotche pamoto zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Musadzalakelake siliva ndi golide wawo kapena kutenga zinthu zimenezi kuti zikhale zanu,+ kuopera kuti zingakutchereni msampha, chifukwa zinthu zimenezi ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.+