Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi kumalo amenewo pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ ndipo muzidzasangalala ndi zochita zanu zonse+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.

  • 2 Mbiri 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino zimene Yehova anachitira Davide, Solomo ndiponso anthu ake Aisiraeli.+

  • Nehemiya 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya ndiponso kukasangalala kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena