Nehemiya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya+ ndi kukondwera kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+
12 Choncho anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya+ ndi kukondwera kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+