Nehemiya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya ndiponso kukasangalala kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+
12 Ndiyeno anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya ndiponso kukasangalala kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+