Yesaya 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa chitowe chakuda sachipuntha ndi chida chopunthira,+Ndipo pachitowe chamtundu wina sayendetsapo mawilo a ngolo yopunthira mbewu. Mʼmalomwake, chitowe chakuda amachipuntha ndi ndodo,Ndipo chitowe chamtundu wina amachipuntha ndi kamtengo.
27 Chifukwa chitowe chakuda sachipuntha ndi chida chopunthira,+Ndipo pachitowe chamtundu wina sayendetsapo mawilo a ngolo yopunthira mbewu. Mʼmalomwake, chitowe chakuda amachipuntha ndi ndodo,Ndipo chitowe chamtundu wina amachipuntha ndi kamtengo.