-
Numeri 26:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho ana aamuna a Yuda mwa mabanja awo anali awa: Shela+ amene anali kholo la banja la Ashela, Perezi+ amene anali kholo la banja la Aperezi ndi Zera+ amene anali kholo la banja la Azera. 21 Ana aamuna a Perezi anali Hezironi+ amene anali kholo la banja la Ahezironi ndi Hamuli+ amene anali kholo la banja la Ahamuli.
-