2 Samueli 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Upite mʼmafuko onse a Isiraeli kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ ndipo ukawerenge anthu kuti ndidziwe chiwerengero chawo.” 2 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira mʼmawa mpaka nthawi yomwe anakonza, moti anthu 70,000 anafa,+ kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ 1 Mbiri 21:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Yowabu sanawerenge anthu a fuko la Levi ndi la Benjamini,+ chifukwa mawu a mfumu anamunyansa kwambiri.+ 7 Zinthu zimenezi sizinasangalatse Mulungu woona ndipo anapha Aisiraeli.
2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Upite mʼmafuko onse a Isiraeli kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ ndipo ukawerenge anthu kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”
15 Kenako Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira mʼmawa mpaka nthawi yomwe anakonza, moti anthu 70,000 anafa,+ kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+
6 Koma Yowabu sanawerenge anthu a fuko la Levi ndi la Benjamini,+ chifukwa mawu a mfumu anamunyansa kwambiri.+ 7 Zinthu zimenezi sizinasangalatse Mulungu woona ndipo anapha Aisiraeli.