Genesis 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Mulungu anamuuza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo mupite ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.” Genesis 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Abulahamu anatchula malowo dzina lakuti Yehova-yire.* Nʼchifukwa chake mpaka lero pali mawu akuti: “Mʼphiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+
2 Kenako Mulungu anamuuza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo mupite ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”
14 Choncho Abulahamu anatchula malowo dzina lakuti Yehova-yire.* Nʼchifukwa chake mpaka lero pali mawu akuti: “Mʼphiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+