Genesis 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu anapitiriza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo muyende ulendo wopita ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:2 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 232/1/2009, tsa. 188/15/2007, tsa. 137/1/1989, ptsa. 21-223/1/1989, tsa. 16
2 Mulungu anapitiriza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo muyende ulendo wopita ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”+
22:2 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 232/1/2009, tsa. 188/15/2007, tsa. 137/1/1989, ptsa. 21-223/1/1989, tsa. 16