Ekisodo 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Lamulo la Pasika ndi ili: Mlendo* asadye nawo.+ Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la Pasika wa Yehova.+ Deuteronomo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo muzipereka nsembe ya Pasika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Muzipereka nkhosa ndi ngʼombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+ 2 Mbiri 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yosiya anachitira Yehova Pasika+ ku Yerusalemu ndipo iwo anapha nyama ya nsembe+ ya Pasika pa tsiku la 14 la mwezi woyamba.+
5 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la Pasika wa Yehova.+
2 Ndipo muzipereka nsembe ya Pasika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Muzipereka nkhosa ndi ngʼombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+
35 Yosiya anachitira Yehova Pasika+ ku Yerusalemu ndipo iwo anapha nyama ya nsembe+ ya Pasika pa tsiku la 14 la mwezi woyamba.+