Salimo 130:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Ya,* mukanakhala kuti mumayangʼanitsitsa* zolakwa,Ndi ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+ Salimo 143:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,Chifukwa palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+
2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,Chifukwa palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+