Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, chonde mvetserani pemphero la ine mtumiki wanu ndiponso pemphero la atumiki anu amene amaopa dzina lanu ndi mtima wonse. Chonde, ndithandizeni ine mtumiki wanu kuti zinthu zindiyendere bwino lero ndipo munthuyu andichitire chifundo.”+

      Pa nthawiyi ndinali woperekera zakumwa kwa mfumu.+

  • Nehemiya 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Komanso kwa zaka 12, kuchokera tsiku limene ndinaikidwa kukhala bwanamkubwa wawo+ mʼdziko la Yuda, kuyambira chaka cha 20+ mpaka chaka cha 32+ cha mfumu Aritasasita,+ ine ndi abale anga sitinadye chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa.+

  • Nehemiya 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amene anatsimikizira panganoli ndi chidindo chawo+ anali awa:

      Nehemiya amene anali bwanamkubwa,* mwana wa Hakaliya,

      Zedekiya,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena