Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 11:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Panalibe mzinda winanso umene unagwirizana za mtendere ndi Aisiraeli, kupatulapo Ahivi a ku Gibiyoni.+ Aisiraeli anamenyana ndi mizinda ina yonse nʼkuigonjetsa.+

  • 2 Samueli 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho mfumu inaitana Agibiyoni+ ndi kulankhula nawo. (Agibiyoni sanali Aisiraeli koma Aamori+ omwe anatsala. Aisiraeli analumbirira Agibiyoni kuti sawapha,+ koma Sauli ankafuna kuwapha onse chifukwa cha mtima wofunitsitsa kuthandiza Aisiraeli ndi Ayuda.)

  • Nehemiya 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako Melatiya wa ku Gibiyoni+ ndi Yadoni wa ku Meronoti anapitiriza kuchokera pamene Yoyada ndi Mesulamu analekezera. Amenewa anali amuna a ku Gibiyoni ndi Mizipa+ amene anali pansi pa ulamuliro wa bwanamkubwa wakutsidya la Mtsinje.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena