Nehemiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu. Nehemiya 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Anthu a fuko la Benjamini anakhala ku Geba,+ ku Mikimasi, ku Aiya, ku Beteli+ ndi midzi yake yozungulira, Nehemiya 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 ku Lodi ndiponso ku Ono,+ chigwa cha amisiri.
2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu.
31 Anthu a fuko la Benjamini anakhala ku Geba,+ ku Mikimasi, ku Aiya, ku Beteli+ ndi midzi yake yozungulira,