Machitidwe 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chilamulo ndi zimene aneneri analemba zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri a sunagoge anatuma munthu kukawauza kuti: “Abale inu, ngati muli ndi mawu alionse amene angalimbikitse anthuwa, lankhulani.” Machitidwe 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera mʼmabuku a Mose, popeza mabuku amenewa amawerengedwa mokweza mʼmasunagoge sabata lililonse.”+
15 Chilamulo ndi zimene aneneri analemba zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri a sunagoge anatuma munthu kukawauza kuti: “Abale inu, ngati muli ndi mawu alionse amene angalimbikitse anthuwa, lankhulani.”
21 Chifukwa kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera mʼmabuku a Mose, popeza mabuku amenewa amawerengedwa mokweza mʼmasunagoge sabata lililonse.”+