Nehemiya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu onse anasonkhana mogwirizana mʼbwalo lalikulu kutsogolo kwa Geti la Kumadzi.+ Anthuwo anauza Ezara+ wokopera Malemba* kuti abweretse buku la Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova analamula Aisiraeli kuti azitsatira.+ Nehemiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aisiraeli anadzipatula kwa anthu onse omwe sanali Aisiraeli+ ndipo anaimirira nʼkuyamba kuulula machimo awo komanso zolakwa za makolo awo.+
8 Anthu onse anasonkhana mogwirizana mʼbwalo lalikulu kutsogolo kwa Geti la Kumadzi.+ Anthuwo anauza Ezara+ wokopera Malemba* kuti abweretse buku la Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova analamula Aisiraeli kuti azitsatira.+
2 Aisiraeli anadzipatula kwa anthu onse omwe sanali Aisiraeli+ ndipo anaimirira nʼkuyamba kuulula machimo awo komanso zolakwa za makolo awo.+