Numeri 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ine ndapereka kwa ana a Levi chakhumi chilichonse+ mu Isiraeli kuti chikhale cholowa chawo chifukwa cha utumiki umene akuchita, utumiki wapachihema chokumanako.
21 Ine ndapereka kwa ana a Levi chakhumi chilichonse+ mu Isiraeli kuti chikhale cholowa chawo chifukwa cha utumiki umene akuchita, utumiki wapachihema chokumanako.