Numeri 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere? Ndipo ndingathe bwanji kuitanira tsoka anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka?+ Numeri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Balaki anapsera mtima Balamu. Ndiyeno Balaki anawomba mʼmanja mokwiya nʼkuuza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere adani anga,+ koma iwe wawadalitsa kwambiri maulendo atatu onsewa.
8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere? Ndipo ndingathe bwanji kuitanira tsoka anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka?+
10 Kenako Balaki anapsera mtima Balamu. Ndiyeno Balaki anawomba mʼmanja mokwiya nʼkuuza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere adani anga,+ koma iwe wawadalitsa kwambiri maulendo atatu onsewa.