-
Yakobo 5:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Abale, pa nkhani ya kumva zowawa+ ndi kuleza mtima,+ tengerani chitsanzo cha aneneri amene analankhula mʼdzina la Yehova.*+ 11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawaona kuti ndi odala.*+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mukudziwa madalitso amene Yehova* anamupatsa.+ Mukuona nokha kuti Yehova* ndi wachikondi chachikulu komanso wachifundo.+
-