Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 5:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Koma ndikanakhala ine, ndikanakadandaula kwa Mulungu,

      Ndipo ndikanakatula mlandu wanga kwa Mulunguyo,

       9 Kwa Iye amene amachita zinthu zazikulu ndi zosatheka kuzifufuza,

      Zinthu zodabwitsa zosawerengeka.

  • Yobu 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Zikanakhala bwino ukanakonza mtima wako

      Nʼkutambasula manja ako kwa iye.

  • Yobu 22:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ukabwerera kwa Wamphamvuyonse, udzabwezeretsedwa mwakale.+

      Ngati utachotsa zosalungama mutenti yako,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena