Yobu 8:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ngati iweyo utayangʼana kwa Mulungu,+Nʼkuchonderera Wamphamvuyonse kuti akuchitire chifundo, 6 Ndipo ngati ukanakhaladi woyera komanso ngati umachitadi zoyenera,+Iye akanakumvera*Ndipo akanakubwezeretsa mmene unalili poyamba.
5 Koma ngati iweyo utayangʼana kwa Mulungu,+Nʼkuchonderera Wamphamvuyonse kuti akuchitire chifundo, 6 Ndipo ngati ukanakhaladi woyera komanso ngati umachitadi zoyenera,+Iye akanakumvera*Ndipo akanakubwezeretsa mmene unalili poyamba.