Yobu 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nʼchifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene wasochera,Amene Mulungu wamutchingira njira?+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo. Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.
23 Nʼchifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene wasochera,Amene Mulungu wamutchingira njira?+
8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo. Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.