Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+
8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+