Mateyu 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+ Yohane 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wodana ndi ine amadananso ndi Atate wanga.+
22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+