Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 19:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iye waika abale anga enieni kutali ndi ine,+

      Ndipo ngakhale anthu ondidziwa andisiya.

  • Yobu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+

      Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+

  • Salimo 31:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+

      Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+

      Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+

      Akandiona ndili panja amandithawa.+

  • Salimo 142:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Yang’anani kudzanja lamanja ndipo muone

      Kuti palibe aliyense amene akufuna kundithandiza.+

      Ndilibenso malo othawirako,+

      Ndipo palibe amene akufunsa za moyo wanga.+

  • Luka 23:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Komanso onse amene anali kumudziwa anaimirira chapatali ndithu.+ Ndipo amayi amene anamutsatira kuchokera ku Galileya, anaimiriranso chapomwepo n’kumaonerera zinthu zimenezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena