Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+ Salimo 69:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha chitonzo, ndipo chilonda chake ndi chosachiritsika.+Ndinali kuyembekezera kuti wina andimvere chifundo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndinali kuyembekezera onditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+
11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+
20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha chitonzo, ndipo chilonda chake ndi chosachiritsika.+Ndinali kuyembekezera kuti wina andimvere chifundo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndinali kuyembekezera onditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+
8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+